Коранът на Chichewa / Chinyanja офлайн ikupezeka tsopano па интернет.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja / Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa / Chinyanja.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.
Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba a mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga копирайте и поставете kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Просто щракнете дълго, за да копирате и поставите)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.